-
Yeremiya 49:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa wanena kuti, ‘Ine ndikukubweretserani chinthu chochititsa mantha,
Kuchokera kwa anthu onse amene akuzungulirani.
Mudzabalalitsidwa kulowera mbali zonse,
Ndipo palibe amene adzasonkhanitse anthu amene athawa.’”
-