-
Yeremiya 49:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 “Taona! Wina adzabwera ngati mkango+ kuchokera munkhalango zowirira zamʼmphepete mwa Yorodano. Adzabwera kudzaukira malo otetezeka odyetserako ziweto, koma mʼkanthawi kochepa ndidzamuthamangitsa pamalowo. Ndidzaika pamalopo mtsogoleri amene ndamusankha. Chifukwa ndi ndani amene angafanane ndi ine ndipo ndi ndani angatsutsane nane? Kodi pali mʼbusa amene angakane kuchita zimene ine ndikufuna?+
-