Yeremiya 49:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Ine ndikuthyola uta wa Aelamu,+ umene umachititsa kuti akhale amphamvu.*
35 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Ine ndikuthyola uta wa Aelamu,+ umene umachititsa kuti akhale amphamvu.*