-
Yeremiya 49:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 “Aelamu ndidzawachititsa mantha pamaso pa adani awo ndi pamaso pa anthu amene akufunafuna moyo wawo. Ndidzawabweretsera tsoka, mkwiyo wanga woyaka moto,” akutero Yehova. “Ndidzawatumizira lupanga mpaka nditawawononga onse.”
-