Yeremiya 50:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo adzafunsira njira yopita ku Ziyoni nkhope zawo zitayangʼana kumeneko.+ Iwo adzanena kuti, ‘Bwerani, tiyeni tikhalenso anthu a Yehova pochita pangano limene lidzakhalapo mpaka kalekale lomwe silidzaiwalika.’+
5 Iwo adzafunsira njira yopita ku Ziyoni nkhope zawo zitayangʼana kumeneko.+ Iwo adzanena kuti, ‘Bwerani, tiyeni tikhalenso anthu a Yehova pochita pangano limene lidzakhalapo mpaka kalekale lomwe silidzaiwalika.’+