Yeremiya 50:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mayi wanu wachititsidwa manyazi.+ Mayi amene anakuberekani wakhumudwa. Taonani! Iye ndi wosafunika kwenikweni pakati pa mitundu ina,Iye ali ngati dera lopanda madzi ndiponso chipululu.+
12 Mayi wanu wachititsidwa manyazi.+ Mayi amene anakuberekani wakhumudwa. Taonani! Iye ndi wosafunika kwenikweni pakati pa mitundu ina,Iye ali ngati dera lopanda madzi ndiponso chipululu.+