Yeremiya 50:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova watsegula nyumba yake yosungiramo zida,Ndipo akutulutsamo zida zimene amagwiritsa ntchito posonyeza mkwiyo wake.+ Chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa, ali ndi ntchito yoti achiteMʼdziko la Akasidi.
25 Yehova watsegula nyumba yake yosungiramo zida,Ndipo akutulutsamo zida zimene amagwiritsa ntchito posonyeza mkwiyo wake.+ Chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa, ali ndi ntchito yoti achiteMʼdziko la Akasidi.