Yeremiya 50:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Bwerani mudzamuukire kuchokera mʼmadera akutali.+ Tsegulani nkhokwe zake.+ Muunjikeni pamodzi ngati milu ya tirigu. Mumuwonongeretu.+ Mʼdzikomo musapezeke aliyense wotsala.
26 Bwerani mudzamuukire kuchokera mʼmadera akutali.+ Tsegulani nkhokwe zake.+ Muunjikeni pamodzi ngati milu ya tirigu. Mumuwonongeretu.+ Mʼdzikomo musapezeke aliyense wotsala.