Yeremiya 50:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Aisiraeli komanso Ayuda akuponderezedwa,Ndipo anthu onse amene anawagwira nʼkupita nawo kudziko lina akuwakakamira.+ Akukana kuwalola kuti abwerere kwawo.+
33 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Aisiraeli komanso Ayuda akuponderezedwa,Ndipo anthu onse amene anawagwira nʼkupita nawo kudziko lina akuwakakamira.+ Akukana kuwalola kuti abwerere kwawo.+