Yeremiya 50:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho nyama zamʼchipululu zidzakhala mmenemo pamodzi ndi nyama zolira mokuwa,Ndipo nthiwatiwa zidzakhala mmenemo.+ Mumzindawo simudzakhalanso munthu aliyense,Ndipo sudzakhala malo oti munthu nʼkukhalamo ku mibadwo yonse.”+
39 Choncho nyama zamʼchipululu zidzakhala mmenemo pamodzi ndi nyama zolira mokuwa,Ndipo nthiwatiwa zidzakhala mmenemo.+ Mumzindawo simudzakhalanso munthu aliyense,Ndipo sudzakhala malo oti munthu nʼkukhalamo ku mibadwo yonse.”+