Yeremiya 51:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Tinayesetsa kuti tichiritse Babulo koma sanachiritsike. Musiyeni, tiyeni tizipita. Aliyense apite kudziko lakwawo.+ Chifukwa zolakwa zake zafika kumwamba,Zafika pamwamba kwambiri ngati mitambo.+
9 “Tinayesetsa kuti tichiritse Babulo koma sanachiritsike. Musiyeni, tiyeni tizipita. Aliyense apite kudziko lakwawo.+ Chifukwa zolakwa zake zafika kumwamba,Zafika pamwamba kwambiri ngati mitambo.+