Yeremiya 51:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye ndi Mulungu amene anapanga dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu zake,Amene anakhazikitsa dziko lapansi pogwiritsa ntchito nzeru zake+Amenenso anatambasula kumwamba chifukwa cha kuzindikira kwake.+
15 Iye ndi Mulungu amene anapanga dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu zake,Amene anakhazikitsa dziko lapansi pogwiritsa ntchito nzeru zake+Amenenso anatambasula kumwamba chifukwa cha kuzindikira kwake.+