-
Yeremiya 51:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Ndidzakugwiritsa ntchito pophwanya mwamuna ndi mkazi.
Ndidzakugwiritsa ntchito pophwanya mwamuna wachikulire ndi kamnyamata.
Ndidzakugwiritsa ntchito pophwanya mnyamata ndi mtsikana.
-