Yeremiya 51:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Babulo adzakhala milu yamiyala,+Malo obisalamo mimbulu,+Chinthu chochititsa mantha komanso chimene anthu azidzachiimbira mluzuNdipo simudzapezeka munthu wokhalamo.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:37 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,6/2017, tsa. 3
37 Babulo adzakhala milu yamiyala,+Malo obisalamo mimbulu,+Chinthu chochititsa mantha komanso chimene anthu azidzachiimbira mluzuNdipo simudzapezeka munthu wokhalamo.+