Yeremiya 51:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Anthu onse pamodzi adzabangula ngati mikango yamphamvu.* Adzalira ngati ana a mikango.”