-
Yeremiya 51:46Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
46 Musataye mtima kapena kuchita mantha ndi uthenga umene udzamveke mʼdzikoli.
Mʼchaka chimodzi uthenga udzafika,
Kenako mʼchaka chotsatira kudzabweranso uthenga wina,
Wonena za chiwawa chimene chidzachitike mʼdzikoli komanso wonena kuti wolamulira akuukira wolamulira mnzake.
-