Yeremiya 51:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Inu amene mwathawa lupanga, pitirizani kuthawa, musaime.+ Kumbukirani Yehova pamene muli kutali kwambiri,Ndipo muziganizira Yerusalemu mumtima mwanu.”+
50 Inu amene mwathawa lupanga, pitirizani kuthawa, musaime.+ Kumbukirani Yehova pamene muli kutali kwambiri,Ndipo muziganizira Yerusalemu mumtima mwanu.”+