Yeremiya 52:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mʼchaka cha 18 cha ulamuliro wa Nebukadinezara,*+ anthu 832 anatengedwa kuchokera ku Yerusalemu.