Maliro 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ulemerero wonse wa mwana wamkazi wa Ziyoni* wamuchokera.+ Akalonga ake ali ngati mbawala zamphongo zimene zikusowa msipu,Ndipo akuyenda mofooka pamaso pa amene akuwathamangitsa.
6 Ulemerero wonse wa mwana wamkazi wa Ziyoni* wamuchokera.+ Akalonga ake ali ngati mbawala zamphongo zimene zikusowa msipu,Ndipo akuyenda mofooka pamaso pa amene akuwathamangitsa.