Maliro 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Machimo anga amangidwa mʼkhosi mwanga ngati goli. Iye wawamanga mwamphamvu ndi dzanja lake. Aikidwa mʼkhosi mwanga moti mphamvu zanga zatha. Yehova wandipereka mʼmanja mwa anthu amene sindingathe kulimbana nawo.+ Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:14 Nsanja ya Olonda,9/1/1988, tsa. 26
14 Machimo anga amangidwa mʼkhosi mwanga ngati goli. Iye wawamanga mwamphamvu ndi dzanja lake. Aikidwa mʼkhosi mwanga moti mphamvu zanga zatha. Yehova wandipereka mʼmanja mwa anthu amene sindingathe kulimbana nawo.+