Maliro 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova ndi wolungama,+ koma ine ndapandukira malamulo ake.*+ Mvetserani, inu anthu a mitundu yonse ndipo muone ululu umene ndikumva. Anamwali* anga ndi anyamata anga atengedwa kupita ku ukapolo.+ Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:18 Nsanja ya Olonda,9/1/1988, tsa. 26
18 Yehova ndi wolungama,+ koma ine ndapandukira malamulo ake.*+ Mvetserani, inu anthu a mitundu yonse ndipo muone ululu umene ndikumva. Anamwali* anga ndi anyamata anga atengedwa kupita ku ukapolo.+