Maliro 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthu amva mmene ndikuusira moyo, koma palibe aliyense woti anditonthoze. Adani anga onse amva za tsoka langa. Iwo akusangalala chifukwa inu mwatibweretsera tsoka.+ Koma inu mubweretsadi tsiku limene munanena,+ kuti iwowo adzakhale ngati ine.+
21 Anthu amva mmene ndikuusira moyo, koma palibe aliyense woti anditonthoze. Adani anga onse amva za tsoka langa. Iwo akusangalala chifukwa inu mwatibweretsera tsoka.+ Koma inu mubweretsadi tsiku limene munanena,+ kuti iwowo adzakhale ngati ine.+