Maliro 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova waphimba mwana wamkazi wa Ziyoni* mumtambo wa mkwiyo wake. Iye waponya pansi kukongola kwa Isiraeli kuchokera kumwamba kupita padziko lapansi.+ Sanakumbukire chopondapo mapazi ake+ pa tsiku la mkwiyo wake. Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:1 Nsanja ya Olonda,6/1/2007, ptsa. 8-99/1/1988, tsa. 26
2 Yehova waphimba mwana wamkazi wa Ziyoni* mumtambo wa mkwiyo wake. Iye waponya pansi kukongola kwa Isiraeli kuchokera kumwamba kupita padziko lapansi.+ Sanakumbukire chopondapo mapazi ake+ pa tsiku la mkwiyo wake.