Maliro 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye wathetsa mphamvu zonse za* Isiraeli atakwiya kwambiri. Adani athu atatiukira, iye sanatithandize,+Ndipo mkwiyo wakewo unapitiriza kuyakira Yakobo ngati moto umene wawononga chilichonse chimene chili pafupi.+
3 Iye wathetsa mphamvu zonse za* Isiraeli atakwiya kwambiri. Adani athu atatiukira, iye sanatithandize,+Ndipo mkwiyo wakewo unapitiriza kuyakira Yakobo ngati moto umene wawononga chilichonse chimene chili pafupi.+