Maliro 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo ankafunsa amayi awo kuti: “Kodi chakudya ndi vinyo zili kuti?”+ Pamene ankakomoka mʼmabwalo a mzinda ngati munthu amene wavulazidwa,Ndiponso pamene moyo wawo unkachoka ali mʼmanja mwa mayi awo.
12 Iwo ankafunsa amayi awo kuti: “Kodi chakudya ndi vinyo zili kuti?”+ Pamene ankakomoka mʼmabwalo a mzinda ngati munthu amene wavulazidwa,Ndiponso pamene moyo wawo unkachoka ali mʼmanja mwa mayi awo.