-
Maliro 3:56Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
56 Imvani mawu anga. Musatseke khutu lanu pamene ndikulira kupempha kuti mundithandize komanso kuti mundipatse mpumulo.
-