Maliro 3:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Inu Yehova, mwaona zoipa zimene andichitira. Chonde, ndiweruzeni mwachilungamo.+