Maliro 3:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Inu Yehova, mwamva mawu awo onyoza ndipo mwaona ziwembu zawo zonse zimene andikonzera.+