-
Maliro 3:62Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
62 Mwamva mawu ochokera pakamwa pa anthu amene akundipondereza. Mwamvanso ziwembu zimene akunongʼonezana tsiku lonse kuti andichitire.
-