-
Maliro 4:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ana okondedwa a Ziyoni amene anali amtengo wapatali ngati golide woyengedwa bwino,
Tsopano akuonedwa ngati mitsuko ikuluikulu yadothi,
Ntchito ya manja a munthu woumba mbiya.
-