Maliro 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ngakhale mimbulu imapereka bere kwa ana ake kuti ayamwe,Koma mwana wamkazi wa anthu anga wakhala wankhanza+ ngati nthiwatiwa zamʼchipululu.+ Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:3 Nsanja ya Olonda,6/1/2007, ptsa. 10-119/1/1988, tsa. 27
3 Ngakhale mimbulu imapereka bere kwa ana ake kuti ayamwe,Koma mwana wamkazi wa anthu anga wakhala wankhanza+ ngati nthiwatiwa zamʼchipululu.+