Maliro 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu amene ankadya chakudya chabwino agona mʼmisewu chifukwa cha njala.+ Anthu amene ankavala zovala zamtengo wapatali+ kuyambira ali ana, agona pamilu yaphulusa.
5 Anthu amene ankadya chakudya chabwino agona mʼmisewu chifukwa cha njala.+ Anthu amene ankavala zovala zamtengo wapatali+ kuyambira ali ana, agona pamilu yaphulusa.