Ezekieli 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atalankhula nane, mzimu unalowa mwa ine ndipo unandipangitsa kuti ndiimirire+ kuti ndizitha kumva zomwe amene ankalankhula ndi ineyo ankanena. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2022, tsa. 4
2 Atalankhula nane, mzimu unalowa mwa ine ndipo unandipangitsa kuti ndiimirire+ kuti ndizitha kumva zomwe amene ankalankhula ndi ineyo ankanena.