Ezekieli 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ukawauze mawu anga, kaya akamvetsera kapena ayi, chifukwa iwo ndi anthu opanduka.+