Ezekieli 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atautambasula, ndinaona kuti mpukutuwo unali wolembedwa kumbali zonse.+ Mumpukutumo munalembedwa nyimbo zoimba polira, mawu odandaula ndi mawu olira.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:10 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2022, tsa. 6
10 Atautambasula, ndinaona kuti mpukutuwo unali wolembedwa kumbali zonse.+ Mumpukutumo munalembedwa nyimbo zoimba polira, mawu odandaula ndi mawu olira.+