-
Ezekieli 3:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Chifukwa sindikukutuma kwa anthu amene amalankhula chilankhulo chovuta kumva kapena chilankhulo chimene iwe sukuchidziwa, koma ndikukutuma ku nyumba ya Isiraeli.
-