Ezekieli 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako mzimu unanditenga+ ndipo ndinayamba kumva mawu amphamvu kumbuyo kwanga ngati chimkokomo chachikulu akuti: “Ulemerero wa Yehova utamandike kumalo amene amakhala.”
12 Kenako mzimu unanditenga+ ndipo ndinayamba kumva mawu amphamvu kumbuyo kwanga ngati chimkokomo chachikulu akuti: “Ulemerero wa Yehova utamandike kumalo amene amakhala.”