Ezekieli 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako ndinamva phokoso la mapiko a angelo pamene mapikowo ankakhulana.+ Ndinamvanso phokoso la mawilo amene anali pambali pawo+ komanso chimkokomo chachikulu.
13 Kenako ndinamva phokoso la mapiko a angelo pamene mapikowo ankakhulana.+ Ndinamvanso phokoso la mawilo amene anali pambali pawo+ komanso chimkokomo chachikulu.