Ezekieli 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iweyo ukachenjeza munthu woipa koma iye osasiya zoipa zakezo ndi njira zake zoipa, munthuyo adzafa chifukwa cha zolakwa zake, koma iweyo udzapulumutsadi moyo wako.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:19 Nsanja ya Olonda,3/15/1991, tsa. 15
19 Iweyo ukachenjeza munthu woipa koma iye osasiya zoipa zakezo ndi njira zake zoipa, munthuyo adzafa chifukwa cha zolakwa zake, koma iweyo udzapulumutsadi moyo wako.+