Ezekieli 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma ndikamalankhula nawe ndizikutsegula pakamwa ndipo iweyo uziwauza kuti,+ ‘Izi nʼzimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa wanena.’ Wakumva amve,+ ndipo amene sakufuna kumva asamve, chifukwa iwo ndi anthu opanduka.”+
27 Koma ndikamalankhula nawe ndizikutsegula pakamwa ndipo iweyo uziwauza kuti,+ ‘Izi nʼzimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa wanena.’ Wakumva amve,+ ndipo amene sakufuna kumva asamve, chifukwa iwo ndi anthu opanduka.”+