Ezekieli 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndidzafuna kuti uchite zimenezi kwa masiku 390, mogwirizana ndi zaka za kulakwa kwawo.+ Ndipo iweyo udzanyamula zolakwa za nyumba ya Isiraeli. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:5 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 12
5 Ine ndidzafuna kuti uchite zimenezi kwa masiku 390, mogwirizana ndi zaka za kulakwa kwawo.+ Ndipo iweyo udzanyamula zolakwa za nyumba ya Isiraeli.