Ezekieli 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Udzakwanitse masiku onsewo. Kenako udzagonere kumanja kwako, ndipo udzanyamule zolakwa za nyumba ya Yuda+ kwa masiku 40. Ndakupatsa tsiku limodzi kuti liimire chaka chimodzi. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:6 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 32 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 12
6 Udzakwanitse masiku onsewo. Kenako udzagonere kumanja kwako, ndipo udzanyamule zolakwa za nyumba ya Yuda+ kwa masiku 40. Ndakupatsa tsiku limodzi kuti liimire chaka chimodzi.