Ezekieli 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nkhope yako izidzayangʼana Yerusalemu+ atazunguliridwa ndi asilikali. Udzapinde malaya ako kuti dzanja lako lidzakhale pamtunda ndipo udzalosere zinthu zoipa zimene zidzachitikire mzindawo.
7 Nkhope yako izidzayangʼana Yerusalemu+ atazunguliridwa ndi asilikali. Udzapinde malaya ako kuti dzanja lako lidzakhale pamtunda ndipo udzalosere zinthu zoipa zimene zidzachitikire mzindawo.