Ezekieli 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsiku lililonse uzidzadya chakudya chochita kuyeza. Uzidzadya chakudya chokwana masekeli 20.* Uzidzadya chakudyachi nthawi yofanana tsiku lililonse. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:10 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 12
10 Tsiku lililonse uzidzadya chakudya chochita kuyeza. Uzidzadya chakudya chokwana masekeli 20.* Uzidzadya chakudyachi nthawi yofanana tsiku lililonse.