Ezekieli 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Uzidzamwa madzi ochita kuyeza, ndipo uzidzamwa makapu awiri okha.* Uzidzamwa madziwo nthawi yofanana tsiku lililonse. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:11 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 12
11 Uzidzamwa madzi ochita kuyeza, ndipo uzidzamwa makapu awiri okha.* Uzidzamwa madziwo nthawi yofanana tsiku lililonse.