-
Ezekieli 4:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Uzidzadya chakudyacho ngati mmene umadyera mkate wozungulira wa balere. Uzidzachiphika iwo akuona pogwiritsa ntchito tudzi touma ta anthu.”
-