Ezekieli 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova anapitiriza kunena kuti: “Mofanana ndi zimenezi, Aisiraeli azidzadya chakudya chodetsedwa pakati pa anthu a mitundu ina kumene ndidzawabalalitsireko.”+
13 Yehova anapitiriza kunena kuti: “Mofanana ndi zimenezi, Aisiraeli azidzadya chakudya chodetsedwa pakati pa anthu a mitundu ina kumene ndidzawabalalitsireko.”+