-
Ezekieli 4:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Choncho iye anandiuza kuti: “Chabwino, ndikulola kuti uzigwiritsa ntchito ndowe za ngʼombe mʼmalo mwa tudzi ta anthu kuti uziphikira chakudya chako.”
-