Ezekieli 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova komanso kuti zimene ndinanena kuti ndidzawabweretsera tsoka limeneli, sizinali nkhambakamwa chabe.”’+
10 Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova komanso kuti zimene ndinanena kuti ndidzawabweretsera tsoka limeneli, sizinali nkhambakamwa chabe.”’+