Ezekieli 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu anthu amene mukukhala mʼdzikoli, mapeto anu afika.* Nthawi ikubwera, tsiku lake layandikira.+ Mʼmapiri mukumveka phokoso lachisokonezo, osati lachisangalalo. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:7 Nsanja ya Olonda,7/1/2007, tsa. 119/15/1988, tsa. 13
7 Inu anthu amene mukukhala mʼdzikoli, mapeto anu afika.* Nthawi ikubwera, tsiku lake layandikira.+ Mʼmapiri mukumveka phokoso lachisokonezo, osati lachisangalalo.